Nasho nyirenda anabadwa pa 25 February, 1982 ndipo m’banja mwawo anabadwa ana 7 ndipo iye ndi omaliza kubadwa.

Nasho anayamba kuyimba mu family choir mpaka kuzayamba gulu lotchedwa Christ Melodies lomwe linajambula zimbale zingapo mpaka kudzafika poyamba kuyimba yekha.
Nasho adatulutsa chimbale chimodzi chotchedwa Zatheka chomwe chinatuluka mu chaka cha 2017 ndipo kuchokera pomwepo Nasho wakhala akutulutsa ma single koma chimbale chake chachiwiri chituluka pompano chotchedwa Zatheka vol 2.
Kupatula kuyimba Nasho ndi Sales Technician Ku Puma ndipo amakhala ku Ndirande mumzinda wa Blantyre.
1 comment
Keep up the good work!