Home » KUCHEZA_NDI_MONTFORT_JENALA (MJ MONTY)

KUCHEZA_NDI_MONTFORT_JENALA (MJ MONTY)

by Harris Msosa
106 views

Montfort Jenala yemwe pamayimbidwe amadziwika ndi dzina lakuti MJ Monty anabadwa pa 12 April, 1985 ndipo m’banja mwawo anabadwa ana asanu ndipo iye ndi wachinayi kubadwa ndipo amakhala ku area 47 mumzinda wa Lilongwe.

“Montfort anayamba kuyimba mu chaka cha 2008, “Ndimapeka nyimbo koma danga la studio m’nalibe kamba ka mapezedwe a ndalama koma patapita zaka m’nayamba kupezako ndalama kenako ndinakumana ndi Albert Khoza amenenso ndi oyimba komanso producer amene ndinamuyimbila akapela nyimbo ziwili mwa nyimbo zanga mpamene amati tiye ndikujambule chimbale ndipo kuyimba kunayambila pompo” Adatero Montfort.

Pakadali pano Montfort watulutsako zimbale zinayi ndipo mitu ya zimbalezi ndi monga Tikondane, Kachi Malawi, I believe komanso I’m Blessed chomwe ndi chimbale chatsopano chomwe chituluke ndikukhazikitsidwa mu mwezi wa June chaka chino.

Kupatula kuyimba Montfort ndi wa business komanso ali ndi company ndipo ndi Managing Director wa Nana’s Investment komanso L&L Cleaning & Landscaping services.

Spread the love

Follow Us

More Songs From Kucheza_ndi_montfort_jenala (mj

Leave a Comment

malawigospelmusic.com is a Christian music website with all Malawian gospel Music and any gospel News.malawigospelmusic.com offer services like song lyrics,Audio upload,poems,Music video upload on our You Tube channel called Malawian Gospel Music, Artist biography, Extended playlist (EP),Article, Album and Banner on website. For inquiry contact these numbers 0888 069 117/0885 572 836 or 0983 592 032/0994 56 15 46 or info@malawigospelmusic.com

All Rights Reserved – Designed and Developed by Kay Dee Media