Given Mulenga anabadwa pa 12 February 1992,School yake ya primary anaphunzira ku Chaba FP School P/O Box 86 Chitipa, Malawi kenaka anakapitiriza maphunziro ake ku Enukweni CDSS Mzimba.
Kuchoka pamenepo anamva maitanidwe a ubusa ndipo anapanga theology ku Malawi Assembless of God Institute Theology MAGIT.Asanayambe utumiki Mulungu anamupatsa mphatso ya kuyimba ndipo anayamba kuyimba 2009 kufikira 2023 ndipo anatulutsa chimbale (Title of Album Chomwe Wadzala) Given Mulenga ndi okwatila ali ndi mkazi wotchedwa Rabecca Banda ndipo ali ndi ana awiri Chisomo ndi Faith.