Baxfull Joseph Nefutary (B. J. N) anabadwa pa 15 April, 1987 ndipo anayamba kuyimba mu chaka cha 2021.M’banja mwawo anabadwa ana 9 koma 5 adamwalira adatsala ana 4 ndipo iye …
All Rights Reserved – Designed and Developed by Kay Dee Media
Baxfull Joseph Nefutary (B. J. N) anabadwa pa 15 April, 1987 ndipo anayamba kuyimba mu chaka cha 2021.M’banja mwawo anabadwa ana 9 koma 5 adamwalira adatsala ana 4 ndipo iye …
Frank Nkhwazi anabadwa pa 3 March 1984 ndipo m’banja mwawo anabadwa ana 9 ndipo iye ndi oyamba. Frank anayamba kuyimba ali wachichepere ali standard 5 kenako luso lidapitilira mpaka pano.Pakadali …
Yobu Bazale Kachitenji anabadwa pa 1 January 1999 ndipo m’banja la kwawo anabadwa ana 5 ndipo iye ndi wa number 4. Yobu anayamba kuyimba m’chaka cha 2017 ndipo pa chiyambi …
Given Mulenga anabadwa pa 12 February m’chaka cha 1992 ndipo ndiwachiwiri kubadwa m’banja la ana atatu. Kuyimba anayamba mu chaka cha 2018.watulutsapo chimbale chimodzi mutu wake “Chomwe Wadzala”.Choyamba nyimbo zanga …
Chimwemwe Mandala amachokera m’mudzi mwa Samuti T/A Chimaliro m’boma la Thyolo ndipo anabadwa m’chaka cha 1987. Chimwemwe anayamba kuyimba kale kwambiri ali mwana koma mbuyo monsemu zimakhala zovutirapo kwa iye …
Mike Wawoh Alibewawoh anabadwa pa 14 May 1986 ndipo m’banja mwawo mwana ndiyekha. Mike anayamba kuyimba mu chaka cha 2000 ndipo adatulutsapo chimbale chake choyamba mu 2007 ndipo anadzayikhazikitsa ku …
Gelson Mahala anabadwa pa 14 may 1999 ku chipatala cha Malamulo T/A Khwethemule, Thyolo ndipo pano amakhalira m’mudzi mwa Jekete mfumu yayikulu Mpama boma la Chiradzulu. M’banja lawo anabadwamo ana …
Ruth Chijani Zaipa anabadwa pa 24 May 1984, kwa bambo anabadwa ana awiri ndipo kwa mayi anabadwa ana asanu ndi m’modzi atsikana okhaokha ndipo konseku iye ndi oyamba kubadwa. Anayamba …
Costance Faith Kapanda anabadwa pa 19 September, 1994 ndipo m’banja mwawo anabadwa ana 4 ndipo iye ndi womaliza. Faith anayamba kuyimba m’chaka cha 2010 pamene adali ku sukulu ndipo pomufunsa …
Grace Kantwanje Kwilasi whose stage name is Grace Wokonderedwa was born in 1984 and released his first single in 2016. They are 7 in their family and she is number …
malawigospelmusic.com is a Christian music website with all Malawian gospel Music and any gospel News.malawigospelmusic.com offer services like song lyrics,Audio upload,poems,Music video upload on our You Tube channel called Malawian Gospel Music, Artist biography, Extended playlist (EP),Article, Album and Banner on website. For inquiry contact these numbers 0888 069 117/0885 572 836 or 0983 592 032/0994 56 15 46 or info@malawigospelmusic.com
All Rights Reserved – Designed and Developed by Kay Dee Media