-
Clement Maungena “BK Boy” born on 12 September 1982 in Machinga district. He is from Balaka district, Batamila 2, T\A Nsamala. He is a Mechanical engineer and a musician and …
-
James Gulule ndi woimba,mtumiki (Evangelist) komanso mphunzitsi yemwe adabadwa pa 4 April,1992.Ndi mwana woyamba kubadwa m’banja la kwawo momwe muli ana 9 (amuna 4 ndipo akazi 5).Ndiokwatira ndipo ali ndi …
-
Camillius Simakweri anabadwila ku chileka m’boma la Blantyre ndipo anakulira ku Zimbabwe komwe anachita maphunziro ake a primary.Banja la kwawo anabadwa ana atatu ( kumbali ya amayi )ndipo ana 5 …
-
The group is based in Liwonde township in Machinga district. The group started in 2016 and by then made a collaboration with Liwonde Christ Ambassadors Choir under Malawi Assemblies of …
-
Cephas Kachingwe amachokela kwa T/A Ganya m’mudzi mwa chimowa m’boma la Ntcheu ndipo anabadwa pa 05-12-1983, iye ndi mwana wa chiwiri m’banja lomwe munabadwaso ana awiri.Pakadali pano amakhala ku Lilongwe …
-
Mabvuto Panganani anabadwa mu Chaka cha 1982 mu banja la ana 4 mwa ana atatu ndi akazi wamamuna alipo yekha komanso wotsiliza pobadwa woyamba kubadwa ndi Teleza kenako Tikalipo ndikubwera …
-
Lameck Soko was born on 7th April,1975 in the City of Blantyre at QueenElizabeth Central Hospital (Q.E.C.H) He is from Semion Mvula Village, T / A Mbelwa V, in Mzimba. …
-
Chris Makondetsa, known professionally as ChrisMaks, is a Malawian singer, songwriter, composer, and pastor. Born on October 28, 1993 in Mulanje, Malawi,he is the first born in a family of …
-
Ada Simeon Chirwa anabadwa mubanja la ana 5 ndipo iyeyo ndi wa chiwili.Anabadwa pa11,01,1988 koma ana onse akadali ndi moyo.Kumudzi kwawo ndiku nkhatabay,Liuzi area, m’mudzi wa adamba liuzi. Anakwatilapo koma …
-
Chosen Man anabadwa pa(6/9/1992 ndipo kumudzi ndi ku Phalombe koma anabadwila ku M’chinji komwe kunali makolo nthawi imeneyo koma pakadali pano akukhalira ku Johannesburg m’dziko la South Africa. Atakulako msinkhu …
-
Angozo James Matemba amachokera Kwa Bvumbwe ku Thyolo koma wakulila Ku Blantyre Chigumula m’mudzi otchedwa Chiwaya. Anabadwila ku Mulambala m’mudzi mwa amfumu Agunde chipatala cha Anambado mu chaka cha 1986 …
-
JOSAM TOLETSANI MASINAANABADWILA KU NTCHEU T/A GANYA PA 1 JUNE 1979 NDIPO AMAPEZEKA KU MALEMBO M’MUDZI MWA KUCHILIMBA T/A NANKUMBA M’BOMA LA MANGOCHI. M’BANJA MWAWO ANABADWA ANA 7 0NSE ALIPO …
-
Nathan Simba was born on 28 June 1989 at mangochi hospital.Fourth born son in a family of five (Three boys and two girls. Nathan Simba anabadwila ndi kukulila ku Mangochi …
-
Maggie Wamkachisi Maurice is a third born daughter in a family of 3 ,They are all girls..Maggie comes from Ndalama village in Dowa district. She is 44 years of age …
All Rights Reserved – Designed and Developed by Kay Dee Media