-
NAME: RICHARD MASANKHA BANDA AGE: 45 HOME VILLAGE : MCHINJI, T/A MLONYENI, MSELERA VILLAGE He was born and grew up in Mchinji, Lilongwe, Mulanje and Thyolo. He did his primary …
-
Hope Bonjesi anabadwa komanso kukulira ku Chikwawa M’mudzi mwa Buneta T/A Masache.Anabadwa pa 23/11/1992,ndipo ndiwoyamba kubadwa m’banja la ana anayi. M’chaka cha 2013 anayamba kulemba nkhani zomwe amaziwerenga pa assembly …
-
Artness Ngalauka kubadwila ku Dedza m’mudzi mwa a Mfutso,kukulila ku Lilongwe ku Chilinde.Artness anabadwa pa 29 September 1983, mwana oyamba kubadwa m’banja la ana 4,akazi okhaokha. Maitanidwe amayimbidwe anamufikila ali …
-
Pastor Paul S Phiri was born on 15 January 1981 in a family of 7 brothers and 1 sister but 2 brothers are late.Right now they are 6 of them.He …
-
Paul Phiri anabadwa pa 12 December 1997 ku Lilongwe pa chipatala cha Bottom.Paul ndiwoyamba kubadwa ku banja la malemu mai ndi bambo Phiri, pamutu pake panaponda ana 4 omwe m’modzi …
-
The servant of God Mirriam Chipwaila anabadwira ku Mangochi kwa Mfumu Katuli,pachipatala cha Chigweje.Anabadwa pa 26/09/1986 ndipo m’banja mwawo anabadwa ana okwana 9 akazi asanu ndipo amuna anayi.The servant of …
-
Born on 19th September 1986 at Bottom hospital now called Bwaila hospital in Lilongwe.He started his music journey in primary school and his first song to record was YANKHO which …
-
Blessed Nellie Mwale ndi M’busa wa Malawi Assemblies of God ndipo anabadwira ku Nkhotakota koma anakulira ku Lilongwe.Anabadwa pa 8/11/1987, m’banja mwawo anabadwa ana 5 ,Iyeyo ndi wa number 2 …
-
Ruth Misomali Serious Man anabadwira ku Chikwawa M’mudzi ndirande kukulira konko komanso ku Mulanje.Anabadwa pa 19 November 1991 ndipo m’banja mwawo anabadwa ana okwana 5 akazi atatu ndi amuna awili …
-
Saini Misoya anabadwa m’mudzi wa Sole, kuchididi boma la Nsanje.Saini Misoya anabadwa pa 14 February 1982,ndipo iyeyu anabadwa mubanja la ana khumi(10)ndipo ndimwana oyamba kubadwa. Saini Misoya anayamba kuimba ali …
-
Favour Chimpini Mkwamba anabadwa pa 5 /12/1995 ku Blantyre komaso kukulira Ku Blantyre komweko ndipo m’banja mwawo anabadwa ana okwana 8 koma omwe adatsala amoyo ndi 7 m’modzi adamwalira ndipo …
-
Mike Wiseman Tembo anabadwa pa 1 January 1989 Ku Chilimba Nkairo ndipo akulira kuchilimba komweko ndi Ku Nsanje pa Phokera T/A Mbenje chifukwa mayi ake anachita kulowoledwa koma pano amakhalira …
-
The Devil Challengers ndi gulu lomwe muli anyamata oyimba awiri ndipo anyamata amenewa mayina awo ndi Joel Majuni komaso Elijah Njirayagoma. Joel ndi ochokera m’mudzi mwa Rhoda mfumu yayikulu Kunthembwe/Chileka …
-
Patrick Makhumula was born in 1979 on 11 October and he is from Blantyre,Mdeka and his home village is Nthache village T/A Chugaru. He was born in a family of …
All Rights Reserved – Designed and Developed by Kay Dee Media