Yembekezani Kandadza anabadwa pa 3/3/1972 m’mudzi mwa Chiwaza T/A Chauma m’boma la Dedza.
Anayamba kuyimba m’chaka cha 1995 pamene anayambitsa limodzi band,wayimbapo Chosen Warriors Band,Biriwita Mbenjere Band ndipo pano ali mu new Stars Celebrations.
Watulutsa zimbale zokwana 5 ma collections wayimba ndi anthu osiyanasiyana.