Weston Chitsulo anabwadwira boma la Thyolo ndipo school waphunzila ku Blantyre.waimbapo kwaya zaka zambiri kufikira panopa.
Anayamba kuyimba 2014 nthawi imeneyo amakonda za sekera ndipo nthawi imeneyo amakonda kucheza ndi Douglas Khangiwa. 2017 anayamba kujambulitsa gospel music. 2021 pa 5 December anali ndi launch ku Turffontein C.C.A.P Church South Africa. panopa wayamba kujambulitsa volume 2 ndipo nyimbo zonse wajambula ndi Chimwemwe Jere.