Home » SAINI MISOYA – BIOGRAPHY

SAINI MISOYA – BIOGRAPHY

by Malawi Gospel Music
116 views

Saini Misoya anabadwa m’mudzi wa Sole, kuchididi boma la Nsanje.Saini Misoya anabadwa pa 14 February 1982,ndipo iyeyu anabadwa mubanja la ana khumi(10)ndipo ndimwana oyamba kubadwa.

Saini Misoya anayamba kuimba ali wachichepere maka mumakwaya ndipo mu chaka cha 2022 ndipomwe anayamba kujambula nyimbo zake zomwe pano zikumveka m’ma wailesi ena aku malawi.

Saini Misoya amakonda kwambiri zamaimbidwe chifukwa chachidwi chakechi mu 2021 anapangitsapo mpikisano wamaimbidwe omwe umadziwika kuti Misoya records gospel music competition,ndipo mu mpikisano umenewu munalowa makwaya okwana 20 ndipo number 1,2 ndi 3 ndi omwe analandira mphoto monga Keyboard ndi ndalama.Cholinga champikisanowu chinali kukweza ndikufunanso kuti uthenga wa Mulungu ufike patali kudzela m’maimbidwe.

Spread the love

Follow Us

More Songs From Saini misoya

Leave a Comment

malawigospelmusic.com is a Christian music website with all Malawian gospel Music and any gospel News.malawigospelmusic.com offer services like song lyrics,Audio upload,poems,Music video upload on our You Tube channel called Malawian Gospel Music, Artist biography, Extended playlist (EP),Article, Album and Banner on website. For inquiry contact these numbers 0888 069 117/0885 572 836 or 0983 592 032/0994 56 15 46 or info@malawigospelmusic.com

All Rights Reserved – Designed and Developed by Kay Dee Media