Home » RUTH MISOMALI SERIOUS MAN – BIOGRAPHY

RUTH MISOMALI SERIOUS MAN – BIOGRAPHY

by Malawi Gospel Music
315 views

Ruth Misomali Serious Man anabadwira ku Chikwawa M’mudzi ndirande kukulira konko komanso ku Mulanje.Anabadwa pa 19 November 1991 ndipo m’banja mwawo anabadwa ana okwana 5 akazi atatu ndi amuna awili iye ndi wa number 3.Atagobadwa anapatsidwa dzina loti Elida ndipo atasinkhuka adazisitha kudzitcha Ruth.

Maitanidwe amaimbidwe anayamba ali wachichepele pomwe amakonda kunvera nyimbo za gospel kwambili and chidwi chinakulilakulira pomwe anadzakwatiwa ndi woyimba komanso producer malemu sir Serious Man.Ruth ali ndi ana atatu anyamata okha okha Happy 13 years ,Praise ndi Promise 9 years mapasa.

Spread the love

Follow Us

More Songs From Ruth misomali

Leave a Comment

malawigospelmusic.com is a Christian music website with all Malawian gospel Music and any gospel News.malawigospelmusic.com offer services like song lyrics,Audio upload,poems,Music video upload on our You Tube channel called Malawian Gospel Music, Artist biography, Extended playlist (EP),Article, Album and Banner on website. For inquiry contact these numbers 0888 069 117/0885 572 836 or 0983 592 032/0994 56 15 46 or info@malawigospelmusic.com

All Rights Reserved – Designed and Developed by Kay Dee Media