Home » LUKE NYONI – BIOGRAPHY

LUKE NYONI – BIOGRAPHY

by Malawi Gospel Music
192 views

Luke Nyoni anabadwila komaso kukulira ku Mzimba T/A Mtwalo.Anabadwa pa 14 /12/1992 m’banja la ana 6 ndipo iye ndi wa number 4 m’modzi wanamba 3 anamwalira.

Atabadwa dzina anamupatsa Luke Nyoni abambo ake ndipo anayamba kuimba nyimbo chifukwa anaona kuti ndimbali imodzi yofalitsila uthenga wa Mulungu kwa anthu ambiri.Luke ndi okwatira ndipo ali ndi mkazi ndi mwana m’modzi pakadali pano ndipo ali m’dziko la South Africa ku Johannesburg.

Spread the love

Follow Us

More Songs From Luke nyoni

Leave a Comment

malawigospelmusic.com is a Christian music website with all Malawian gospel Music and any gospel News.malawigospelmusic.com offer services like song lyrics,Audio upload,poems,Music video upload on our You Tube channel called Malawian Gospel Music, Artist biography, Extended playlist (EP),Article, Album and Banner on website. For inquiry contact these numbers 0888 069 117/0885 572 836 or 0983 592 032/0994 56 15 46 or info@malawigospelmusic.com

All Rights Reserved – Designed and Developed by Kay Dee Media