Born on 30 November 1990, at Matawale hospital in Zomba, fifth born daughter of Mr and Mrs Chimombo, married with two children a boy and a girl, khumbo lake ndikufuna kufalitsa ndikulalikira kudzera m’mayimbidwe kufikira tsiku la kudza kwa Ambuye,cholinga chakuyimba akufuna kuti anthu ambiri akapulumutsidwe akamudziwe Yesu Khristu mkudzera m’mayimbidwe ake.
School yake waphunzira kwambiri pa Kanjedza Primary School in Blantyre,Secondary ku Joshua Pvt koma sanapite nayo patali pa zifukwa zina chifukwa waleledwa kwambiri ndi alamu ake omwe anali wa police ku PMF ku Blantyre.Wayimbapo choir ku PTS mu CCAP kuyambira chaka cha 2002 ali ndi zaka 10,wayimbaponso praise team mu Living Water ku South Africa.
Anayamba kuyimba yekha as solo artist mu chaka cha 2021 pa 1 February ataona masomphenya kwa kanthawi, pambali poti iye ndi otumikira mkuyimba ndi Evangelist nso koma as of now alibe church amapemphera mpingo wa Living Faith Ministry in South Africa, album yoyamba anatulutsa pa 6 March, 2022 yomwe mutu wake Ndi Yehova Ndiye M’busa Wanga.