Home » ELISHA MBENDERA – BIOGRAPHY

ELISHA MBENDERA – BIOGRAPHY

by Malawi Gospel Music
227 views

Elisha Mbendera ndilo dzina lake lapa msonkho.Anabadwa mu chaka cha 1987 ndipo amakondwerera tsiku lakubadwa kwake pa 6 september.

Anabadwa m’banja la Bambo ndi Mayi Mbendera pomwe anabereka ana okwana 8 ndipo iye ndi wachitatu kubadwa.

Kumudzi kwawo ndi ku Ntcheu T/A Mpando, village headman Songayi koma pano wakulira akukhala ku Lilongwe.Ndi mkhristu ndipo amapemphera ku Zambezi Evangelical Church.

Kuyimba anayamba mkale kuchokera ku choir ndipo anachitika chisomo kukhalanso m’modzi wa m’nyamata odziwa kupanga backing oyimba ochuluka maka a Gospel kuno ku Malawi komanso ma international artists omwe amakhala kuti abwera mu dziko muno.

Watulutsa chimbale chimodzi chomwe chikutchedwa KULI YAHWE chomwe chikunyamula ma hit like LAKOMA BWANJI TCHIMOLO, MUKUCHITA KUMWETULIRA (Chikumbu Mtima), Wadzuka, Dziko laweruza Maso ndi Maso, Uzimu umachoka, Mundigwire dzanja, Ndimasulidwe ft Evance Mereka, Adonai komanso Ndaona.Ndi okwatira ali ndi mwana m’modzi wamamuna dzina lake Maziko Elishen Mbendera.

Spread the love

Follow Us

More Songs From Elisha mbendera

Leave a Comment

malawigospelmusic.com is a Christian music website with all Malawian gospel Music and any gospel News.malawigospelmusic.com offer services like song lyrics,Audio upload,poems,Music video upload on our You Tube channel called Malawian Gospel Music, Artist biography, Extended playlist (EP),Article, Album and Banner on website. For inquiry contact these numbers 0888 069 117/0885 572 836 or 0983 592 032/0994 56 15 46 or info@malawigospelmusic.com

All Rights Reserved – Designed and Developed by Kay Dee Media