Home » CEPHAS KACHINGWE – BIOGRAPHY

CEPHAS KACHINGWE – BIOGRAPHY

by Malawi Gospel Music
296 views

Cephas Kachingwe amachokela kwa T/A Ganya m’mudzi mwa chimowa m’boma la Ntcheu ndipo anabadwa pa 05-12-1983, iye ndi mwana wa chiwiri m’banja lomwe munabadwaso ana awiri.Pakadali pano amakhala ku Lilongwe kuchokela m’chaka cha 1992.

Cephas Kachingwe anayamba kuyimba m’chaka Cha 1998 pamene amayimba nawo choir yontchedwa Chisomo, kuchokela m’chaka cha 2000 Cephas anayamba kupeka nyimbo zomwe choir yi imayimba kufikila lero lino.Kupatula pa khani ya mayimbidwe Cephas Kachingwe amagwila ntchito ya zomangamanga ndipo ali ndi m’kazi m’modzi komanso ana atatu amuna awiri Misheck ndi Miracle ndi wamkazi Tabitha.

Spread the love

Follow Us

More Songs From Cephas kachingwe

Leave a Comment

malawigospelmusic.com is a Christian music website with all Malawian gospel Music and any gospel News.malawigospelmusic.com offer services like song lyrics,Audio upload,poems,Music video upload on our You Tube channel called Malawian Gospel Music, Artist biography, Extended playlist (EP),Article, Album and Banner on website. For inquiry contact these numbers 0888 069 117/0885 572 836 or 0983 592 032/0994 56 15 46 or info@malawigospelmusic.com

All Rights Reserved – Designed and Developed by Kay Dee Media