Home » BLESSED NELLIE MWALE – BIOGRAPHY

BLESSED NELLIE MWALE – BIOGRAPHY

by Malawi Gospel Music
140 views

Blessed Nellie Mwale ndi M’busa wa Malawi Assemblies of God ndipo anabadwira ku Nkhotakota koma anakulira ku Lilongwe.Anabadwa pa 8/11/1987, m’banja mwawo anabadwa ana 5 ,Iyeyo ndi wa number 2 pobadwa ndipo Pastor Nellie Mwale Sali pabanja pakadali pano.

Maitanidwe a maimbidwe anamufikira ali mwana.Abambo ake amkaimba voice komanso guitar ndipo sunday lililonse amakaimba ku tsogolo ku church ndipo akakhala kunyumba abambo ake madzulo alionse amaimba ndi ana awo kuphatikizapo Nellie ndipo abambowo amapeka okha nyimbo komanso kuimba.Nellie anayamba kupeka nyimbo ali ndi zaka 15 ndipo mu 2009 anatulutsa album yotchedwa Ndamdziwa Yesu.

Spread the love

Follow Us

More Songs From Blessed nellie

Leave a Comment

malawigospelmusic.com is a Christian music website with all Malawian gospel Music and any gospel News.malawigospelmusic.com offer services like song lyrics,Audio upload,poems,Music video upload on our You Tube channel called Malawian Gospel Music, Artist biography, Extended playlist (EP),Article, Album and Banner on website. For inquiry contact these numbers 0888 069 117/0885 572 836 or 0983 592 032/0994 56 15 46 or info@malawigospelmusic.com

All Rights Reserved – Designed and Developed by Kay Dee Media