Home » ROSE MWALURE – BIOGRAPHY

ROSE MWALURE – BIOGRAPHY

by Malawi Gospel Music
413 views

ROSE CHARLES MWALURE ANABADWA 1985 PA 2 JANUARY PA CHIPATALA CHA PA CHONDE BOMA LA MULANJE. NDIPO AMACHOKELA BOLA LOMWELO LA MULANJE T/A NTHILAMANJA MUDZI MWAKHAYANO. ANABADWA MUBANJA LA ANA 4 NDIPO NDI IYE NDI OYAMBA KUBADWA NDIPO MWANA WA MKAZI NDI IYE YEKHA.

MAYI AKE ANALI OLIVE SIMON MULIMA AMENE ANAMWALIRA 2006 NDIPO ANASIYA ANA 4 AMASIYE MUTHAWI IMENEYO ALERANA ANA OKHA OKHA
NDIPO PANO ROSE ALI NDI ANA AWIRI TIONGE GONDWE NDI PATRICIA GONDWE NDI ZIDZUKULU ZIWIRI TRUST NDI NICIA.

WAKULA MOVUTIKA KWAMBIRI BANJA LOSAUKA KOMANSO WALELEDWA OPANDA BAMBO. KUIMBA ANAYAMBA ALI WA WA CHICHEPELE PAMENE AMAIMBA CHOIR YA MENDULO PALISH KOMANSO ST PAUL LOLO CATHOLIC LUCHENZA. KUIMBA PAYEKHA ANAYAMBA 2017 PAMENE ANALOWA MU STUDIO KU MALAWI ASANABWELELE KU SOUTH AFRICA. ROSE NDI BORN AGAIN ANALANDILA YESU KHRISTU MU CHAKA CHA 2010 ATANGOMWALIRA AGOGO AKE NDIPO IZI ZINACHITIKA ATAPANGA NGOZI NDI FIRST BORN WAKE POMWE TRUCK IDAWAGUNDA KUGWELA KUNSI KWA BRIDGE KOMA AMBUYE ADAWAPULUMUTSA.

ALI NDI CHIMBALE CHIMENE WACHITULUTSA ONLY CD MU APRIL 2022 PANALI PA 3 CHIMBALECHI CHIMATCHEDWA NDILI NDIMATHA. PANO ALINSO NDI MA MUSIC VIDEO OCHEPA OMWE AKUPEZEKA PA YOU TUBE NDIPO DVD ITULUKA POSAKHALITSAPA. AMAKHALA KU CAPETOWN NDIPO AKUTHA 6 YEARS, ROSE NDI OSAKWATIWA NDIPO KU CAPE TOWN ANABWELERA KUSAKA MA GANYU KUTI MOYO UZIFEWA PANGONO.

Spread the love

You may also like

Leave a Comment

malawigospelmusic.com is a Christian music website with all Malawian gospel Music and any gospel News.malawigospelmusic.com offer services like song lyrics,Audio upload,poems,Music video upload on our You Tube channel called Malawian Gospel Music, Artist biography, Extended playlist (EP),Article, Album and Banner on website. For inquiry contact these numbers 0888 069 117/0885 572 836 or 0983 592 032/0994 56 15 46 or info@malawigospelmusic.com

All Rights Reserved – Designed and Developed by Kay Dee Media