Frank Nkhwazi anabadwa pa 3 March 1984 ndipo m’banja mwawo anabadwa ana 9 ndipo iye ndi oyamba.
Frank anayamba kuyimba ali wachichepere ali standard 5 kenako luso lidapitilira mpaka pano.Pakadali pano Frank ali ndi zimbale zitatu zomwe zonse zinakhazikitsidwa kale ndipo amachokera ku Rumphi ndipo ndi munthu wa Business.